
Flames yafika kuno kumudzi kuchokera ku South Africa
Timu ya dziko lino ya anyamata ‘The Flames’ yafika mu ulendo wake ochokera mdziko la South Africa komwe inakasewera ndi timu ya dzikolo ya Bafana Bafana Lamulungu. Malawi yabwera koma itausiya mpikisano wa CHAN pa bwalo la Loftus mdziko la South Africa …